Salimo 90:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tichititseni kusangalala kwa masiku ofanana ndi masiku amene mwatisautsa,+Kwa masiku ofanana ndi zaka zimene taona masoka.+ Yeremiya 52:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako anayamba kulankhula naye zinthu zabwino, ndipo anakweza ufumu wake kuposa mafumu ena amene anali naye limodzi ku Babulo.+
15 Tichititseni kusangalala kwa masiku ofanana ndi masiku amene mwatisautsa,+Kwa masiku ofanana ndi zaka zimene taona masoka.+
32 Kenako anayamba kulankhula naye zinthu zabwino, ndipo anakweza ufumu wake kuposa mafumu ena amene anali naye limodzi ku Babulo.+