Genesis 41:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Farao anatuma anthu kukatenga Yosefe+ kundendeko,+ kuti abwere naye mofulumira. Choncho Yosefeyo anameta bwinobwino,+ kenako anasintha zovala+ n’kukaonekera pamaso pa Farao. Genesis 41:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+
14 Tsopano Farao anatuma anthu kukatenga Yosefe+ kundendeko,+ kuti abwere naye mofulumira. Choncho Yosefeyo anameta bwinobwino,+ kenako anasintha zovala+ n’kukaonekera pamaso pa Farao.
42 Atatero, Farao anavula mphete yake yachifumu+ kudzanja lake, n’kuiveka kudzanja la Yosefe. Anamuvekanso malaya amtengo wapatali, ndi tcheni chagolide m’khosi mwake.+