Maliko 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano anthu anayamba kum’bweretsera ana aang’ono kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo anawakalipira.+
13 Tsopano anthu anayamba kum’bweretsera ana aang’ono kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo anawakalipira.+