1 Mafumu 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Eliya anauza mayiyo kuti: “Bweretsa kuno mwana wakoyo.” Ndiyeno anatenga mwanayo m’manja mwa mayi ake n’kupita naye kuchipinda chapadenga.+ Chipinda chimenechi n’chimene Eliya anali kukhalamo, ndipo anagoneka mwanayo pabedi lake.+ Mateyu 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwe popemphera, lowa m’chipinda chako pawekha+ ndi kutseka chitseko, ndipo pemphera kwa Atate wako amene ali kosaoneka.+ Ukatero Atate wako amene amaona kuchokera kosaonekako adzakubwezera.
19 Koma Eliya anauza mayiyo kuti: “Bweretsa kuno mwana wakoyo.” Ndiyeno anatenga mwanayo m’manja mwa mayi ake n’kupita naye kuchipinda chapadenga.+ Chipinda chimenechi n’chimene Eliya anali kukhalamo, ndipo anagoneka mwanayo pabedi lake.+
6 Koma iwe popemphera, lowa m’chipinda chako pawekha+ ndi kutseka chitseko, ndipo pemphera kwa Atate wako amene ali kosaoneka.+ Ukatero Atate wako amene amaona kuchokera kosaonekako adzakubwezera.