1 Mafumu 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atatero, anayamba kufuulira Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wanga,+ kodi mukuchitiranso zoipa mkazi wamasiye amene ndikukhala naye monga mlendo wake, mwa kupha mwana wake?” Yohane 11:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Pamenepo anachotsa chimwalacho. Tsopano Yesu anakweza maso ake kumwamba+ ndi kunena kuti: “Atate, ndikukuyamikani kuti mwandimva.+ Machitidwe 9:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+
20 Atatero, anayamba kufuulira Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wanga,+ kodi mukuchitiranso zoipa mkazi wamasiye amene ndikukhala naye monga mlendo wake, mwa kupha mwana wake?”
41 Pamenepo anachotsa chimwalacho. Tsopano Yesu anakweza maso ake kumwamba+ ndi kunena kuti: “Atate, ndikukuyamikani kuti mwandimva.+
40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+