Aheberi 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Akazi analandira akufa awo amene anauka kwa akufa.+ Koma anthu ena anazunzidwa chifukwa sanalole kusiya chikhulupiriro chawo kuti amasulidwe. Iwo anachita zimenezi kuti adzauke kwa akufa, komwe ndi kuuka kwabwino kwambiri.
35 Akazi analandira akufa awo amene anauka kwa akufa.+ Koma anthu ena anazunzidwa chifukwa sanalole kusiya chikhulupiriro chawo kuti amasulidwe. Iwo anachita zimenezi kuti adzauke kwa akufa, komwe ndi kuuka kwabwino kwambiri.