Salimo 148:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu anyamata+ ndi inunso anamwali,+Inu okalamba+ pamodzi ndi ana.+ Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+
13 Onse, anthu ndi nyama, atamande dzina la Yehova,+Pakuti dzina lake lokhalo lili pamwamba posafikirika.+Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+