Salimo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’kamwa mwa ana aang’ono ndi ana oyamwa mwakhazikitsamo zamphamvu,+Chifukwa cha amene akukuchitirani zoipa.+Mwatero kuti mugonjetse mdani wanu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa.+
2 M’kamwa mwa ana aang’ono ndi ana oyamwa mwakhazikitsamo zamphamvu,+Chifukwa cha amene akukuchitirani zoipa.+Mwatero kuti mugonjetse mdani wanu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa.+