Numeri 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+ Mateyu 26:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pamenepo mkulu wa ansembe anang’amba malaya ake akunja n’kunena kuti: “Wanyoza Mulungu!+ Nanga n’kufunanso mboni zina pamenepa?+ Pano mwadzimvera nokha mmene akunyozera Mulungu.+
6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+
65 Pamenepo mkulu wa ansembe anang’amba malaya ake akunja n’kunena kuti: “Wanyoza Mulungu!+ Nanga n’kufunanso mboni zina pamenepa?+ Pano mwadzimvera nokha mmene akunyozera Mulungu.+