Mateyu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano atafika kufupi ndi khamu la anthu,+ mwamuna wina anamuyandikira, ndipo anam’gwadira ndi kunena kuti: Maliko 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kumenekonso munthu wina wakhate anafika kwa iye, ndipo anagwada pansi ndi kum’dandaulira, kuti: “Ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+ Maliko 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano pamene anali kupita, mwamuna wina anam’thamangira ndi kugwada pamaso pake. Kenako anamufunsa kuti: “Mphunzitsi Wabwino, ndichite chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+
14 Tsopano atafika kufupi ndi khamu la anthu,+ mwamuna wina anamuyandikira, ndipo anam’gwadira ndi kunena kuti:
40 Kumenekonso munthu wina wakhate anafika kwa iye, ndipo anagwada pansi ndi kum’dandaulira, kuti: “Ngati mukufuna, mukhoza kundiyeretsa.”+
17 Tsopano pamene anali kupita, mwamuna wina anam’thamangira ndi kugwada pamaso pake. Kenako anamufunsa kuti: “Mphunzitsi Wabwino, ndichite chiyani kuti ndikapeze moyo wosatha?”+