Ekisodo 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+ Ekisodo 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mukandipangira guwa lansembe lamiyala, musamangire miyala yosema. Mukangosema mwala wa guwalo, ndiye kuti mwaipitsa chinthu chopatulika.+
24 Mundipangire guwa lansembe ladothi,+ ndipo muziperekapo nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zachiyanjano,* nkhosa zanu ndi ng’ombe zanu.+ M’malo onse amene ndidzachititsa dzina langa kukumbukika ndidzabwera kwa inu ndipo ndidzakudalitsani ndithu.+
25 Mukandipangira guwa lansembe lamiyala, musamangire miyala yosema. Mukangosema mwala wa guwalo, ndiye kuti mwaipitsa chinthu chopatulika.+