Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 63:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndipo mfumu idzakondwera mwa Mulungu.+

      Aliyense wolumbira m’dzina la Mulungu adzam’tamanda,+

      Pakuti pakamwa pa anthu olankhula chinyengo padzatsekedwa.+

  • Miyambo 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mlomo wa choonadi+ ndi umene udzakhazikike kwamuyaya,+ koma lilime lachinyengo lidzangokhalapo kwa kanthawi.+

  • Miyambo 12:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Milomo yonama imam’nyansa Yehova,+ koma anthu ochita zinthu mokhulupirika amam’sangalatsa.+

  • Yesaya 59:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti m’manja mwanu mwaipitsidwa ndi magazi,+ ndipo zala zanu zaipitsidwa ndi zolakwa.+ Milomo yanu yanena zabodza. Lilime lanu limangokhalira kunena zinthu zopanda chilungamo.+

  • Hoseya 12:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Efuraimu akupitiriza kunena kuti, ‘Inetu ndalemeradi,+ ndapeza zinthu zamtengo wapatali.+ Palibe amene angapeze cholakwa chachikulu pa ntchito zanga zonse.’+

  • Machitidwe 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamenepo Petulo anamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani awirinu munagwirizana kuti muyese+ mzimu wa Yehova? Taona! Anthu amene anapita kukaika mwamuna wako m’manda ali pakhomo. Iwenso akunyamula ndi kutuluka nawe.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena