Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komanso, Mulungu akhoza kuchititsa kuti kukoma mtima kwake konse kwakukulu kusefukire kwa inu. Choncho nthawi zonse mudzakhala ndi zinthu zokwanira kusamalira zosowa zanu, ndipo mudzakhalanso ndi zinthu zambiri zogwiritsa ntchito pa ntchito iliyonse yabwino.+

  • 2 Atesalonika 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.+ M’malomwake, mwa ntchito yathu imene tinagwira mwakhama ndi thukuta lathu,+ tinagwira ntchito usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena