Ekisodo 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aliyense amene anaopa mawu a Yehova pakati pa atumiki a Farao anaonetsetsa kuti ziweto zake ndi antchito ake athawira m’nyumba.+ Miyambo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wochenjera amene waona tsoka amabisala.+ Koma anthu osadziwa zinthu amene amangopitabe amalangidwa.+
20 Aliyense amene anaopa mawu a Yehova pakati pa atumiki a Farao anaonetsetsa kuti ziweto zake ndi antchito ake athawira m’nyumba.+
12 Wochenjera amene waona tsoka amabisala.+ Koma anthu osadziwa zinthu amene amangopitabe amalangidwa.+