-
Genesis 37:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Munthuyo anati: “Amenewo achoka. Ndinawamva akunena kuti, ‘Tiyeni tipite ku Dotana.’” Pamenepo Yosefe anawalondolabe abale akewo mpaka anakawapeza ku Dotanako.
-