Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 19:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma anachititsa khungu amuna amene anali pakhomo la nyumbawo,+ kuyambira wamng’ono kwambiri mpaka wamkulu koposa,+ moti anthuwo anavutika kufufuza khomo.+

  • Miyambo 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Njira ya oipa ili ngati mdima.+ Iwo sadziwa chimene chimawapunthwitsa.+

  • Yesaya 59:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tikungoyenda ndi khoma ngati anthu akhungu, ndipo tikungofufuzafufuza ngati anthu opanda maso.+ Tapunthwa masanasana ngati kuti tili mu mdima wamadzulo. Pakati pa anthu ojintcha, tikungokhala ngati anthu akufa.+

  • Yohane 9:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndiyeno Yesu ananena kuti: “Ndinabwera m’dziko lino kudzapereka chiweruzo ichi:+ Osaona ayambe kuona,+ ndipo oona akhale akhungu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena