Miyambo 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+ Yesaya 8:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aliyense adzadutsa m’dzikolo akuzunzika ndiponso ali ndi njala.+ Chifukwa chakuti ali ndi njala ndiponso wakwiya, adzatukwana mfumu yake ndi Mulungu+ wake ndipo azidzayang’ana kumwamba. Amosi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira mumzinda, kodi anthu sanjenjemera?+ Kodi tsoka likagwa mumzinda si Yehova amene wachititsa?
3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+
21 Aliyense adzadutsa m’dzikolo akuzunzika ndiponso ali ndi njala.+ Chifukwa chakuti ali ndi njala ndiponso wakwiya, adzatukwana mfumu yake ndi Mulungu+ wake ndipo azidzayang’ana kumwamba.
6 Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira mumzinda, kodi anthu sanjenjemera?+ Kodi tsoka likagwa mumzinda si Yehova amene wachititsa?