Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 27:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yembekezera Yehova.+ Limba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+

      Yembekezera Yehova.+

  • Miyambo 14:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Wosafulumira kukwiya n’ngozindikira zinthu kwambiri,+ koma wokwiya msanga amalimbikitsa uchitsiru.+

  • Miyambo 30:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 kuti ndisakhute kwambiri n’kukukanani+ kuti: “Kodi Yehova ndani?”+ ndiponso kuti ndisasauke n’kukaba ndi kunyozetsa dzina la Mulungu wanga.+

  • 2 Petulo 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+

  • Chivumbulutso 16:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Choncho anthu anapsa ndi kutentha kwakukulu. Koma iwo ananyoza dzina la Mulungu,+ amene ali ndi ulamuliro+ pa miliri imeneyi, ndipo sanalape kuti amupatse ulemerero.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena