2 Mafumu 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehoramu+ mwana wa Ahabu, anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya m’chaka cha 18 cha Yehosafati mfumu ya Yuda, ndipo analamulira kwa zaka 12. 2 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehoramu atangoona Yehu, nthawi yomweyo anam’funsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji+ pali dama la Yezebeli+ mayi ako ndi amatsenga ake ambirimbiri?”+
3 Yehoramu+ mwana wa Ahabu, anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya m’chaka cha 18 cha Yehosafati mfumu ya Yuda, ndipo analamulira kwa zaka 12.
22 Yehoramu atangoona Yehu, nthawi yomweyo anam’funsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji+ pali dama la Yezebeli+ mayi ako ndi amatsenga ake ambirimbiri?”+