Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nahumu 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Taonani mapazi a munthu yemwe akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino.+ Iye akulengeza za mtendere. Iwe Yuda, chita zikondwerero zako.+ Kwaniritsa zimene walonjeza+ chifukwa palibe munthu aliyense wopanda pake amene adzadutsa pakati pako.+ Munthu wopanda pakeyo adzaphedwa.”+

  • 1 Akorinto 10:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Aliyense asamangodzifunira zopindulitsa iye yekha basi,+ koma zopindulitsanso wina.+

  • Afilipi 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Musamaganizire zofuna zanu zokha,+ koma muziganiziranso zofuna za ena.+

  • 1 Atesalonika 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Onetsetsani kuti wina asabwezere choipa pa choipa kwa wina aliyense,+ koma nthawi zonse yesetsani kuchita zabwino kwa okhulupirira anzanu ndi kwa ena onse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena