1 Samueli 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Sauli anazindikira mawu a Davide, ndipo anati: “Kodi ndi mawu ako, mwana wanga Davide?”+ Davide anayankha kuti: “Inde ndi mawu anga, mbuyanga mfumu.” 2 Mafumu 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfumu ya Isiraeli ikuyenda pamwamba pa khoma, mayi wina analankhula mokweza kwa mfumuyo kuti: “Ndithandizeni mbuyanga mfumu!”+ 1 Petulo 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+
17 Pamenepo Sauli anazindikira mawu a Davide, ndipo anati: “Kodi ndi mawu ako, mwana wanga Davide?”+ Davide anayankha kuti: “Inde ndi mawu anga, mbuyanga mfumu.”
26 Mfumu ya Isiraeli ikuyenda pamwamba pa khoma, mayi wina analankhula mokweza kwa mfumuyo kuti: “Ndithandizeni mbuyanga mfumu!”+
17 Lemekezani anthu, kaya akhale amtundu wotani.+ Kondani gulu lonse la abale,+ opani Mulungu,+ lemekezani mfumu.+