2 Mafumu 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku lotsatira, Hazaeli anatenga chofunda n’kuchiviika m’madzi. Kenako anaphimba nacho mfumuyo kumaso+ moti inamwalira,+ ndipo Hazaeli+ anayamba kulamulira m’malo mwake.
15 Tsiku lotsatira, Hazaeli anatenga chofunda n’kuchiviika m’madzi. Kenako anaphimba nacho mfumuyo kumaso+ moti inamwalira,+ ndipo Hazaeli+ anayamba kulamulira m’malo mwake.