Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Davide anagona limodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+

  • 1 Mafumu 11:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Kenako Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide+ bambo ake. Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.

  • 1 Mafumu 14:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pomalizira pake, Rehobowamu anagona ndi makolo ake ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide.+ Mayi ake dzina lawo linali Naama Muamoni.+ Kenako Abiyamu+ mwana wa Rehobowamu anayamba kulamulira m’malo mwake.

  • 2 Mbiri 21:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Patatha zaka ziwiri zathunthu iye akudwala, matumbo ake+ anatuluka ndipo anamwalira ndi matenda oipawa. Anthu ake sanamupserezere zofukiza pa maliro ake ngati mmene anachitira+ pa maliro a makolo ake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena