2 Mafumu 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yehu anakwera galeta ulendo wa ku Yezereeli popeza Yehoramu anali chigonere kumeneko. Ahaziya+ mfumu ya Yuda anali atapita ku Yezereeli komweko kukaona Yehoramu.
16 Tsopano Yehu anakwera galeta ulendo wa ku Yezereeli popeza Yehoramu anali chigonere kumeneko. Ahaziya+ mfumu ya Yuda anali atapita ku Yezereeli komweko kukaona Yehoramu.