-
2 Mafumu 4:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Thamanga ukakumane naye. Ukamufunse kuti: ‘Kodi muli bwino? Mwamuna wanu ali bwanji? Nanga mwana wanu ali bwanji?’” Mayiyo anayankha kuti: “Onse ali bwino.”
-