2 Samueli 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Abisalomu anatumiza akazitape+ m’mafuko onse a Isiraeli ndipo anawauza kuti: “Mukangomva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, munene kuti, ‘Abisalomu wakhala mfumu+ ku Heburoni!’”+ 1 Mafumu 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kumeneko, wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akam’dzoze+ kukhala mfumu ya Isiraeli. Ndiyeno mukalize lipenga+ ndi kunena kuti, ‘Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!’+
10 Ndiyeno Abisalomu anatumiza akazitape+ m’mafuko onse a Isiraeli ndipo anawauza kuti: “Mukangomva kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa, munene kuti, ‘Abisalomu wakhala mfumu+ ku Heburoni!’”+
34 Kumeneko, wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akam’dzoze+ kukhala mfumu ya Isiraeli. Ndiyeno mukalize lipenga+ ndi kunena kuti, ‘Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!’+