1 Mafumu 1:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ m’chihema+ n’kudzoza+ Solomo. Ndiyeno anthuwo anayamba kuliza lipenga ndipo anthu onse anafuula kuti: “Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!”+
39 Tsopano wansembe Zadoki anatenga nyanga ya mafuta+ m’chihema+ n’kudzoza+ Solomo. Ndiyeno anthuwo anayamba kuliza lipenga ndipo anthu onse anafuula kuti: “Mfumu Solomo ikhale ndi moyo wautali!”+