1 Mafumu 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patapita nthawi, anthu mumsasawo anamva kuti: “Zimiri wachitira chiwembu mfumu ndipo waipha.” Choncho tsiku limenelo, Aisiraeli onse omwe anali kumsasako anaveka ufumu Omuri,+ mkulu wa asilikali, kuti akhale mfumu ya Isiraeli. 1 Mafumu 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zimiri atangoona kuti mzindawo walandidwa, anakalowa munsanja yomwe inali panyumba ya mfumu n’kuyatsa nyumbayo iye ali mkati mwake, moti anafera momwemo.+
16 Patapita nthawi, anthu mumsasawo anamva kuti: “Zimiri wachitira chiwembu mfumu ndipo waipha.” Choncho tsiku limenelo, Aisiraeli onse omwe anali kumsasako anaveka ufumu Omuri,+ mkulu wa asilikali, kuti akhale mfumu ya Isiraeli.
18 Zimiri atangoona kuti mzindawo walandidwa, anakalowa munsanja yomwe inali panyumba ya mfumu n’kuyatsa nyumbayo iye ali mkati mwake, moti anafera momwemo.+