1 Mafumu 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera apo, anamanga guwa lansembe la Baala m’kachisi+ wa Baala amene iye anamanga ku Samariya. 1 Mafumu 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Ndilipo ndekha mneneri wa Yehova amene watsala,+ ndekhandekha basi, koma aneneri a Baala alipo 450. 1 Mafumu 18:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Gwirani aneneri a Baala! Muonetsetse kuti pasapezeke wothawa!” Nthawi yomweyo anawagwira, ndipo Eliya anatsetserekera nawo kuchigwa cha Kisoni,+ n’kukawapha kumeneko.+ 2 Mafumu 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anali kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati mmene anachitira bambo ake+ kapenanso mmene anachitira mayi ake. Iye anachotsa chipilala chopatulika+ cha Baala chimene bambo ake anapanga.+
32 Kuwonjezera apo, anamanga guwa lansembe la Baala m’kachisi+ wa Baala amene iye anamanga ku Samariya.
22 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Ndilipo ndekha mneneri wa Yehova amene watsala,+ ndekhandekha basi, koma aneneri a Baala alipo 450.
40 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Gwirani aneneri a Baala! Muonetsetse kuti pasapezeke wothawa!” Nthawi yomweyo anawagwira, ndipo Eliya anatsetserekera nawo kuchigwa cha Kisoni,+ n’kukawapha kumeneko.+
2 Iye anali kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ koma osati ngati mmene anachitira bambo ake+ kapenanso mmene anachitira mayi ake. Iye anachotsa chipilala chopatulika+ cha Baala chimene bambo ake anapanga.+