1 Mafumu 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+ 2 Mafumu 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Sanasiye machimo onse a Yerobowamu mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+
16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+
24 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Sanasiye machimo onse a Yerobowamu mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+