11 Iye anawauza kuti: “Izi ndi zimene mfumu yokulamuliraniyo izidzafuna kwa inu:+ Idzatenga ana anu+ kuti azikayenda m’magaleta*+ ake ndi kukwera pamahatchi*+ ake, ndipo ena mwa ana anuwo azidzathamanga patsogolo pa magaleta ake.+
27 Choncho Mfumu Rehobowamu inapanga zishango zamkuwa m’malomwake, ndipo inazipereka kwa akulu a asilikali othamanga,+ omwe anali alonda a pakhomo la nyumba ya mfumu, kuti aziziyang’anira.+