1 Samueli 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Samueli anauza anthuwo zinthu zimene mfumu iyenera kulandira kwa iwo+ ndipo anazilemba m’buku limene analiika pamaso pa Yehova. Kenako Samueli anauza anthuwo kuti aliyense abwerere kwawo. 2 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho akulu onse+ a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni, ndipo Mfumu Davide anachita nawo pangano+ ku Heburoni pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza+ Davide kukhala mfumu ya Isiraeli.+
25 Zitatero, Samueli anauza anthuwo zinthu zimene mfumu iyenera kulandira kwa iwo+ ndipo anazilemba m’buku limene analiika pamaso pa Yehova. Kenako Samueli anauza anthuwo kuti aliyense abwerere kwawo.
3 Choncho akulu onse+ a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni, ndipo Mfumu Davide anachita nawo pangano+ ku Heburoni pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza+ Davide kukhala mfumu ya Isiraeli.+