2 Samueli 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Seva+ anali mlembi,+ ndipo Zadoki+ ndi Abiyatara+ anali ansembe. 2 Mafumu 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anayamba kuitana mfumu mofuula, ndipo kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika.
18 Kenako anayamba kuitana mfumu mofuula, ndipo kunabwera Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyang’anira banja lachifumu, Sebina+ mlembi, ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika.