19 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, momwe anamenyera nkhondo+ ndi momwe analamulirira, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
34 Nkhani zina zokhudza Yehu ndi zonse zimene anachita, ndiponso zochita zake zonse zamphamvu, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.