Deuteronomo 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Chidzakhala chotembereredwa chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha nthaka yako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+ Hoseya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Yehova, apatseni zimene mukuyenera kuwapatsa.+ Chititsani kuti mimba zawo zizipita padera+ ndiponso mabere awo afote.
18 “Chidzakhala chotembereredwa chipatso cha mimba yako,+ chipatso cha nthaka yako,+ ana a ng’ombe zako ndi ana a nkhosa zako.+
14 Inu Yehova, apatseni zimene mukuyenera kuwapatsa.+ Chititsani kuti mimba zawo zizipita padera+ ndiponso mabere awo afote.