1 Mafumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Davide anagona limodzi ndi makolo ake,+ ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide.+ 2 Mafumu 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atumiki ake amene anamupha anali Yozakara+ mwana wa Simeyati ndi Yehozabadi mwana wa Someri. Choncho anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide pamodzi ndi makolo ake, ndipo Amaziya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
21 Atumiki ake amene anamupha anali Yozakara+ mwana wa Simeyati ndi Yehozabadi mwana wa Someri. Choncho anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide pamodzi ndi makolo ake, ndipo Amaziya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.