Ekisodo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+ Oweruza 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero, iwo anayamba kuchotsa milungu yonse yachilendo pakati pawo+ n’kuyamba kutumikira Yehova,+ moti mtima wake+ unagwidwa ndi chisoni chifukwa cha kuvutika kwa ana a Isiraeli.+ Salimo 106:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mulungu akamva kuchonderera kwawo+Anali kuona kuvutika kwawo.+
7 Yehova anawonjezeranso kuti: “Ndaona nsautso ya anthu anga amene ali ku Iguputo, ndipo ndamva kulira kwawo chifukwa cha amene akuwagwiritsa ntchito mwankhanza. Zoonadi, ndikudziwa bwino zowawa zawo.+
16 Atatero, iwo anayamba kuchotsa milungu yonse yachilendo pakati pawo+ n’kuyamba kutumikira Yehova,+ moti mtima wake+ unagwidwa ndi chisoni chifukwa cha kuvutika kwa ana a Isiraeli.+