2 Mafumu 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Azariya,*+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16,+ n’kumulonga ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+ 2 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anthu onse+ a ku Yuda anatenga Uziya+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, n’kumulonga+ ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+
21 Kenako anthu onse a ku Yuda anatenga Azariya,*+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16,+ n’kumulonga ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+
26 Kenako anthu onse+ a ku Yuda anatenga Uziya+ yemwe pa nthawiyo anali ndi zaka 16, n’kumulonga+ ufumu m’malo mwa bambo ake Amaziya.+