2 Mafumu 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehoahazi anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda motsatira tchimo la Yerobowamu+ mwana wa Nebati, limene anachimwitsa nalo Isiraeli.+ Iye sanapatuke pa tchimolo. 2 Mafumu 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Sanasiye machimo onse a Yerobowamu mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+
2 Yehoahazi anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda motsatira tchimo la Yerobowamu+ mwana wa Nebati, limene anachimwitsa nalo Isiraeli.+ Iye sanapatuke pa tchimolo.
24 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. Sanasiye machimo onse a Yerobowamu mwana wa Nebati amene anachimwitsa nawo Isiraeli.+