Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Atamva zimenezi, mkazi wa Yerobowamu ananyamuka n’kumapita ndipo anafika ku Tiriza.+ Atangofika pakhomo la nyumba yawo, mnyamatayo anamwalira.

  • 1 Mafumu 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Basa atangomva zimenezi, nthawi yomweyo anasiya kumanga Rama+ ndipo anapitiriza kukhala ku Tiriza.+

  • 1 Mafumu 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 M’chaka cha 26 cha Asa mfumu ya Yuda, Ela mwana wa Basa anakhala mfumu ya Isiraeli ku Tiriza kwa zaka ziwiri.

  • 1 Mafumu 16:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako Omuri ndi Aisiraeli onse amene anali naye, anachoka ku Gebetoni n’kupita kukaukira+ mzinda wa Tiriza.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena