2 Mafumu 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anam’chitira chiwembu+ Zekariya n’kumupha+ ku Ibuleamu,+ ndipo iye anayamba kulamulira m’malo mwake.
10 Ndiyeno Salumu mwana wa Yabesi anam’chitira chiwembu+ Zekariya n’kumupha+ ku Ibuleamu,+ ndipo iye anayamba kulamulira m’malo mwake.