Yobu 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuti mfuu yachisangalalo ya anthu oipa sikhalitsa,+Ndiponso kuti kusangalala kwa wampatuko kumakhala kwa kanthawi? Miyambo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu okhala m’dziko akamachimwa pamakhala akalonga ambiri otsatizanatsatizana,+ koma chifukwa cha munthu wozindikira, wodziwa zinthu zoyenera kuchita, kalonga amakhala kwa nthawi yaitali.+
5 Kuti mfuu yachisangalalo ya anthu oipa sikhalitsa,+Ndiponso kuti kusangalala kwa wampatuko kumakhala kwa kanthawi?
2 Anthu okhala m’dziko akamachimwa pamakhala akalonga ambiri otsatizanatsatizana,+ koma chifukwa cha munthu wozindikira, wodziwa zinthu zoyenera kuchita, kalonga amakhala kwa nthawi yaitali.+