1 Mafumu 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zimiri atangoona kuti mzindawo walandidwa, anakalowa munsanja yomwe inali panyumba ya mfumu n’kuyatsa nyumbayo iye ali mkati mwake, moti anafera momwemo.+
18 Zimiri atangoona kuti mzindawo walandidwa, anakalowa munsanja yomwe inali panyumba ya mfumu n’kuyatsa nyumbayo iye ali mkati mwake, moti anafera momwemo.+