Ekisodo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usakhale ndi milungu ina iliyonse+ kupatulapo ine.* 1 Mafumu 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+
16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+