Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Kenako anapanga mabeseni 10+ amkuwa. Beseni lililonse linali lokwana mitsuko* 40, ndipo linali mikono inayi kukula kwake. Pachotengera chilichonse mwa zotengera 10 zija panali beseni limodzi.

  • 2 Mbiri 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye anapanganso mabeseni 10. Anaika mabeseni asanu mbali ya kudzanja lamanja, mabeseni asanu mbali ya kumanzere.+ M’mabeseniwo anali kutsukiramo ndi kutsukuluziramo+ zinthu zokhudzana ndi nsembe yopsereza.+ Ansembe anali kusamba madzi ochokera m’thanki ija.+

  • Yeremiya 52:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma panalibe amene anayeza kulemera kwa mkuwa wa zipilala ziwiri zija,+ chosungiramo madzi chimodzi chija,+ ng’ombe zamkuwa 12+ zija ndi zotengera zokhala ndi mawilo zimene Mfumu Solomo inapangira nyumba ya Yehova.+ Palibe amene anayeza kulemera kwa mkuwa wa ziwiya zonsezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena