Hoseya 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+
15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita dama,+ Yuda asakhale wolakwa+ ndipo anthu inu musabwere ku Giligala.+ Musapitenso ku Beti-aveni+ kapena kulumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo!’+