Salimo 105:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 YAMIKANI Yehova, itanani pa dzina lake,+Lengezani zochita zake pakati pa mitundu ya anthu.+ Salimo 106:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Akolose 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzilimbikira kupemphera.+ Mukhale maso pa nkhani ya kupemphera ndipo mukhale oyamikira.+
106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+