Salimo 106:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndani anganene zinthu zamphamvu zimene Yehova wachita,+Kapena ndani angamutamande mokwanira?+ Salimo 111:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye wakonza zoti ntchito zake zodabwitsa zizikumbukiridwa.+ ח [Chehth]Yehova ndi wachisomo ndiponso wachifundo.+
4 Iye wakonza zoti ntchito zake zodabwitsa zizikumbukiridwa.+ ח [Chehth]Yehova ndi wachisomo ndiponso wachifundo.+