Salimo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+ Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wadzisankhira Yakobo,+Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+ 1 Petulo 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mayi* amene ali ku Babulo,+ wosankhidwa mwapadera ngati inuyo, komanso mwana wanga Maliko,+ akupereka moni.
12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+
13 Mayi* amene ali ku Babulo,+ wosankhidwa mwapadera ngati inuyo, komanso mwana wanga Maliko,+ akupereka moni.