Genesis 28:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mbewu yako ndithu idzachuluka ngati mchenga wa padziko lapansi,+ ndipo ana ako adzafalikira kumadzulo, kum’mawa, kumpoto ndi kum’mwera.+ Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbewu yako, mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso*+ ndithu.
14 Mbewu yako ndithu idzachuluka ngati mchenga wa padziko lapansi,+ ndipo ana ako adzafalikira kumadzulo, kum’mawa, kumpoto ndi kum’mwera.+ Komanso kudzera mwa iwe ndi mwa mbewu yako, mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso*+ ndithu.